Salimo 100:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziwani* kuti Yehova ndi Mulungu.+ Iye ndi amene anatipanga, ndipo ndife ake.+ Ndife anthu ake komanso nkhosa zimene akuweta.+ Yesaya 54:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+
3 Dziwani* kuti Yehova ndi Mulungu.+ Iye ndi amene anatipanga, ndipo ndife ake.+ Ndife anthu ake komanso nkhosa zimene akuweta.+
5 Chifukwa Wokupanga Wamkulu+ ali ngati mwamuna* wako,+Dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+