Salimo 104:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye amamanga zipinda zake pamadzi amumlengalenga+ pogwiritsa ntchito matabwa,Amapanga mitambo kukhala galeta lake,+Amayenda pamapiko a mphepo.+ Aheberi 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu* ndipo amachititsa atumiki ake+ kukhala ngati lawi la moto.”+
3 Iye amamanga zipinda zake pamadzi amumlengalenga+ pogwiritsa ntchito matabwa,Amapanga mitambo kukhala galeta lake,+Amayenda pamapiko a mphepo.+
7 Ndiponso ponena za angelo, iye akuti: “Amachititsa kuti angelo ake akhale amphamvu* ndipo amachititsa atumiki ake+ kukhala ngati lawi la moto.”+