Salimo 119:154 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 154 Nditetezeni pa mlandu wanga* ndipo mundipulumutse.+Ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo mogwirizana ndi lonjezo lanu.* Salimo 143:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo chifukwa cha dzina lanu. Ndipulumutseni mʼmavuto anga, chifukwa ndinu wachilungamo.+
154 Nditetezeni pa mlandu wanga* ndipo mundipulumutse.+Ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo mogwirizana ndi lonjezo lanu.*
11 Inu Yehova, ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo chifukwa cha dzina lanu. Ndipulumutseni mʼmavuto anga, chifukwa ndinu wachilungamo.+