-
Aheberi 12:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Nʼzoona kuti palibe chilango chimene chimakhala chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa. Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere, chomwe ndi chilungamo.
-