1 Mafumu 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Atipatse mtima wofuna kuyenda mʼnjira zake zonse+ komanso kutsatira malamulo ake, malangizo ake ndi ziweruzo zake zimene analamula makolo athu. Salimo 119:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndithandizeni kuti mtima wanga uzikonda zikumbutso zanu,Osati kupeza phindu mwachinyengo.+
58 Atipatse mtima wofuna kuyenda mʼnjira zake zonse+ komanso kutsatira malamulo ake, malangizo ake ndi ziweruzo zake zimene analamula makolo athu.