Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wosangalala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kuti akhale cholowa chake.+ Salimo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa anthu oipa adzaphedwa,+Koma amene akuyembekezera Yehova adzalandira dziko lapansi.+ Salimo 37:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Onani munthu wosalakwa,*Ndipo yangʼanitsitsani munthu wolungama,+Chifukwa tsogolo la munthu ameneyo lidzakhala lamtendere.+ Salimo 146:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wosangalala ndi munthu amene amathandizidwa ndi Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+
12 Wosangalala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kuti akhale cholowa chake.+
37 Onani munthu wosalakwa,*Ndipo yangʼanitsitsani munthu wolungama,+Chifukwa tsogolo la munthu ameneyo lidzakhala lamtendere.+
5 Wosangalala ndi munthu amene amathandizidwa ndi Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+