Salimo 25:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngati munthu amaopa Yehova,+ Iye adzamulangiza njira imene akuyenera kusankha.+ נ [Nun] 13 Moyo wake udzasangalala ndi zinthu zabwino,+Ndipo mbadwa* zake zidzatenga dziko lapansi kuti likhale lawo.+ Salimo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Olungama adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzakhala mmenemo mpaka kalekale.+ Mateyu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Osangalala ndi anthu ofatsa+ chifukwa adzalandira dziko lapansi.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+
12 Ngati munthu amaopa Yehova,+ Iye adzamulangiza njira imene akuyenera kusankha.+ נ [Nun] 13 Moyo wake udzasangalala ndi zinthu zabwino,+Ndipo mbadwa* zake zidzatenga dziko lapansi kuti likhale lawo.+
9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+