Salimo 37:23, 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova akasangalala ndi njira za munthu+Amamusonyeza zoyenera kuchita pa moyo wake.+ 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Chifukwa Yehova wamugwira dzanja kuti amuthandize.*+ Salimo 94:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+
23 Yehova akasangalala ndi njira za munthu+Amamusonyeza zoyenera kuchita pa moyo wake.+ 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Chifukwa Yehova wamugwira dzanja kuti amuthandize.*+
18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa likuterereka,” Chikondi chanu chokhulupirika, inu Yehova, chinapitiriza kundithandiza.+