Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 62:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ana a anthu ali ngati mpweya,

      Ana a anthu ndi malo othawirako osadalirika.+

      Onse pamodzi akaikidwa pasikelo amapepuka kuposa mpweya.+

  • Salimo 118:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Kuthawira kwa Yehova nʼkwabwino

      Kusiyana ndi kudalira anthu.+

       9 Kuthawira kwa Yehova nʼkwabwino

      Kusiyana ndi kudalira akalonga.+

  • Yesaya 2:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kuti zinthu zikuyendereni bwino, siyani kudalira munthu wamba,

      Amene ali ngati mpweya chabe wa mʼmphuno mwake.

      Kodi pali chifukwa chilichonse choti munthu azimudalira?

  • Yeremiya 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Yehova wanena kuti:

      “Wotembereredwa ndi munthu amene amakhulupirira munthu mnzake.+

      Wotembereredwa ndi munthu amene amadalira mphamvu za munthu,+

      Komanso amene mtima wake wapatuka kuchoka kwa Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena