Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 30:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yehova wanena kuti: “Tsoka kwa ana aamuna osamvera,+

      Amene amachita zofuna zawo osati zofuna zanga,+

      Amene amapanga mgwirizano* koma osati motsogoleredwa ndi mzimu wanga,

      Kuti awonjezere tchimo pa tchimo.

       2 Iwo amapita ku Iguputo+ asanandifunse,+

      Kuti akapeze chitetezo kwa Farao*

      Ndiponso kuti akabisale mumthunzi wa Iguputo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena