Salimo 103:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tamandani Yehova, inu angelo ake onse+ amphamvu,Amene amamvera mawu ake komanso kuchita zimene wanena.+ Luka 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwadzidzidzi, panaoneka gulu lalikulu lakumwamba lili limodzi ndi mngeloyo+ ndipo linkatamanda Mulungu kuti:
20 Tamandani Yehova, inu angelo ake onse+ amphamvu,Amene amamvera mawu ake komanso kuchita zimene wanena.+
13 Mwadzidzidzi, panaoneka gulu lalikulu lakumwamba lili limodzi ndi mngeloyo+ ndipo linkatamanda Mulungu kuti: