Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+

      Nʼchifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?

      Nʼchifukwa chiyani simukumva kubuula kwanga?+

  • Mateyu 27:46-49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Cha mʼma 3 kolokomo, Yesu anafuula mwamphamvu kuti: “Eʹli, Eʹli, laʹma sa·bach·thaʹni?” kutanthauza kuti, “Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?”+ 47 Ena mwa anthu amene anaimirira chapomwepo atamva zimenezi anayamba kunena kuti: “Munthuyu akuitana Eliya.”+ 48 Nthawi yomweyo mmodzi wa iwo anathamanga kukatenga siponji nʼkuiviika muvinyo wowawasa ndipo anaiika kubango nʼkumupatsa kuti amwe.+ 49 Koma enawo anati: “Mulekeni! Tione ngati Eliya angabwere kudzamupulumutsa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena