Salimo 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+ Yesaya 65:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+
13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Atumiki anga adzadya, koma inu mudzakhala ndi njala.+ Atumiki anga adzamwa,+ koma inu mudzakhala ndi ludzu. Atumiki anga adzasangalala,+ koma inu mudzachita manyazi.+