Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 45:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chifukwa Yehova,

      Mlengi wakumwamba,+ Mulungu woona,

      Amene anaumba dziko lapansi, amene analipanga ndi kulikhazikitsa mwamphamvu,+

      Amene sanalilenge popanda cholinga,* koma analiumba kuti anthu akhalemo,+ wanena kuti:

      “Ine ndine Yehova ndipo palibenso wina.

  • Mateyu 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Osangalala ndi anthu ofatsa+ chifukwa adzalandira dziko lapansi.+

  • Chivumbulutso 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako ndinamva mawu ofuula kuchokera kumpando wachifumu akuti: “Taonani! Chihema cha Mulungu chili pakati pa anthu ndipo iye azidzakhala nawo. Iwo adzakhala anthu ake ndipo Mulunguyo adzakhala nawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena