Salimo 72:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼmasiku a ulamuliro wake, wolungama zinthu zidzamuyendera bwino,*+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka+ kwa nthawi yonse imene mwezi udzakhalepo. Salimo 119:165 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 165 Anthu amene amakonda chilamulo chanu amakhala ndi mtendere wochuluka,+Palibe chimene chingawakhumudwitse.* Yesaya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje+Ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a mʼnyanja.+
7 Mʼmasiku a ulamuliro wake, wolungama zinthu zidzamuyendera bwino,*+Ndipo padzakhala mtendere wochuluka+ kwa nthawi yonse imene mwezi udzakhalepo.
165 Anthu amene amakonda chilamulo chanu amakhala ndi mtendere wochuluka,+Palibe chimene chingawakhumudwitse.*
18 Zingakhale bwino kwambiri mutamvera malamulo anga!+ Mukatero mtendere wanu udzakhala ngati mtsinje+Ndipo chilungamo chanu chidzakhala ngati mafunde a mʼnyanja.+