Genesis 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yehova anati: “Bwanji ndimuuze Abulahamu zimene ndikufuna kuchita?+ Genesis 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbadwa* zako ngati nyenyezi zakumwamba komanso ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.+ Ndipo mbadwa yako idzalanda mzinda* wa adani ake.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonseAsanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbadwa* zako ngati nyenyezi zakumwamba komanso ngati mchenga wamʼmbali mwa nyanja.+ Ndipo mbadwa yako idzalanda mzinda* wa adani ake.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonseAsanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+