Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pambuyo pake, Mulungu anauza Nowa kuti: “Ndaganiza zowononga anthu onse, chifukwa apangitsa kuti dziko lapansi lidzaze ndi chiwawa. Choncho ndiwawononga limodzi ndi zonse zimene zili padziko lapansi.+

  • Genesis 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako Yehova anati: “Bwanji ndimuuze Abulahamu zimene ndikufuna kuchita?+

  • Salimo 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Anthu amene amaopa Yehova ndi amene amakhala naye pa ubwenzi wolimba,+

      Ndipo amawadziwitsa pangano lake.+

  • Yesaya 42:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Taonani, zinthu zimene ndinaneneratu kalekale zachitika,

      Tsopano ndikulengeza zinthu zatsopano.

      Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+

  • Danieli 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye anandithandiza kuti ndimvetse, ndipo anandiuza kuti:

      “Iwe Danieli, tsopano ndabwera kuti ndikupatse nzeru ndi kukuthandiza kumvetsa zinthu zonsezi.

  • Chivumbulutso 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Chivumbulutso* chimene Yesu Khristu anapereka. Mulungu anamupatsa Chivumbulutso chimenechi+ kuti aonetse akapolo ake+ zinthu zimene zikuyenera kuchitika posachedwapa. Yesu anatumiza mngelo wake kuti adzapereke Chivumbulutsocho kwa kapolo wake Yohane+ pogwiritsa ntchito zizindikiro.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena