Salimo 62:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, iye ndi thanthwe langa komanso amene amandipulumutsa, malo anga othawirako otetezeka.Sindidzagwedezeka.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
6 Ndithudi, iye ndi thanthwe langa komanso amene amandipulumutsa, malo anga othawirako otetezeka.Sindidzagwedezeka.+
2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+