Ekisodo 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+ Salimo 77:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Phokoso la bingu lanu+ linali ngati la mawilo a galeta.Kungʼanima kwa mphezi kunaunika padziko lapansi.+Dziko lapansi linanjenjemera komanso kugwedezeka.+
18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+
18 Phokoso la bingu lanu+ linali ngati la mawilo a galeta.Kungʼanima kwa mphezi kunaunika padziko lapansi.+Dziko lapansi linanjenjemera komanso kugwedezeka.+