Salimo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ine ndine nyongolotsi osati munthu,Anthu amandinyogodola* komanso kundinyoza.+ Salimo 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu amene amadana nane kwambiri akundinyoza,*Amandinyoza tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+ Salimo 102:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsiku lonse adani anga amandinyoza.+ Anthu amene amanditonza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.
10 Anthu amene amadana nane kwambiri akundinyoza,*Amandinyoza tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+
8 Tsiku lonse adani anga amandinyoza.+ Anthu amene amanditonza amagwiritsa ntchito dzina langa potemberera ena.