Miyambo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu amakhala ndi mapulani ambiri mumtima mwake,Koma zolinga za Yehova nʼzimene zidzakwaniritsidwe.+ Yesaya 46:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kutatsala nthawi yaitali, ndimaneneratu zimene zidzachitike,Ndipo kale kwambiri ndinaneneratu zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo.+ Ine ndimanena kuti, ‘Zolinga zanga zidzachitikadi,+Ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+
21 Munthu amakhala ndi mapulani ambiri mumtima mwake,Koma zolinga za Yehova nʼzimene zidzakwaniritsidwe.+
10 Kutatsala nthawi yaitali, ndimaneneratu zimene zidzachitike,Ndipo kale kwambiri ndinaneneratu zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo.+ Ine ndimanena kuti, ‘Zolinga zanga zidzachitikadi,+Ndipo ndidzachita chilichonse chimene ndikufuna.’+