Salimo 73:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi, izi nʼzimene oipa amachita, amakhala mosatekeseka nthawi zonse.+ Iwo amawonjezera chuma chawo.+ Salimo 73:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo awonongedwa mwadzidzidzi.+ Afika pamapeto awo modzidzimutsa ndipo atha momvetsa chisoni!
12 Ndithudi, izi nʼzimene oipa amachita, amakhala mosatekeseka nthawi zonse.+ Iwo amawonjezera chuma chawo.+