Miyambo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu amene sakwiya msanga ndi wozindikira zinthu kwambiri,+Koma wosaugwira mtima amasonyeza uchitsiru wake.+ Aefeso 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati mwakwiya, musachimwe.+ Dzuwa lisalowe mudakali okwiya.+
29 Munthu amene sakwiya msanga ndi wozindikira zinthu kwambiri,+Koma wosaugwira mtima amasonyeza uchitsiru wake.+