Salimo 78:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Anachititsa kuti malo ake opatulika akhalepo mpaka kalekale ngati kumwamba,*+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+ Salimo 104:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye wakhazikitsa dziko lapansi pamaziko ake.+Silidzasunthidwa pamalo ake* mpaka kalekale.+ Salimo 119:90 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwo yonse.+ Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lipitirizebe kukhalapo.+ Miyambo 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anayala maziko a dziko lapansi mwanzeru.+ Anakhazikitsa kumwamba mozindikira.+
69 Anachititsa kuti malo ake opatulika akhalepo mpaka kalekale ngati kumwamba,*+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+
90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwo yonse.+ Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lipitirizebe kukhalapo.+