Salimo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikomereni mtima,* inu Yehova, chifukwa ndayamba kufooka. Ndichiritseni, inu Yehova,+ chifukwa mafupa anga akunjenjemera. Salimo 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinati: “Inu Yehova, ndikomereni mtima.+ Ndichiritseni,+ chifukwa ndakuchimwirani.”+ Salimo 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichititseni kumva kufuula kokondwera ndi kosangalala,Kuti ndisangalale ngakhale kuti mwathyola mafupa anga.+
2 Ndikomereni mtima,* inu Yehova, chifukwa ndayamba kufooka. Ndichiritseni, inu Yehova,+ chifukwa mafupa anga akunjenjemera.
8 Ndichititseni kumva kufuula kokondwera ndi kosangalala,Kuti ndisangalale ngakhale kuti mwathyola mafupa anga.+