1 Samueli 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Samueli anati: “Kodi Yehova amasangalala ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zina+ kuposa kumvera mawu a Yehova? Dikira ndikuuze! Kumvera kumaposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kumaposa mafuta+ a nkhosa zamphongo. Salimo 51:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa nsembe simukuifuna, mukanakhala kuti mukuifuna ndikanaipereka kwa inu.+Inu simusangalala ndi nsembe yopsereza yathunthu.+ 17 Nsembe zimene Mulungu amasangalala nazo ndi kudzimvera chisoni mumtima.Inu Mulungu, simudzakana* mtima wosweka ndi wophwanyika.+ Hoseya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa ndimakondwera ndi chikondi chokhulupirika,* osati nsembe.Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati nsembe zopsereza zathunthu.+
22 Samueli anati: “Kodi Yehova amasangalala ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zina+ kuposa kumvera mawu a Yehova? Dikira ndikuuze! Kumvera kumaposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kumaposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.
16 Chifukwa nsembe simukuifuna, mukanakhala kuti mukuifuna ndikanaipereka kwa inu.+Inu simusangalala ndi nsembe yopsereza yathunthu.+ 17 Nsembe zimene Mulungu amasangalala nazo ndi kudzimvera chisoni mumtima.Inu Mulungu, simudzakana* mtima wosweka ndi wophwanyika.+
6 Chifukwa ndimakondwera ndi chikondi chokhulupirika,* osati nsembe.Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati nsembe zopsereza zathunthu.+