Salimo 74:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,Iye ndi amene amapulumutsa anthu padziko lapansi.+ Yesaya 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+
12 Koma Mulungu ndi Mfumu yanga kuyambira kalekale,Iye ndi amene amapulumutsa anthu padziko lapansi.+
22 Chifukwa Yehova ndi Woweruza wathu,+Yehova ndi Wotipatsa Malamulo,+Yehova ndi Mfumu yathu.+Iye ndi amene adzatipulumutse.+