Salimo 97:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Moto umachoka kwa iye+Nʼkupsereza adani ake omuzungulira.+ 4 Kungʼanima kwa mphezi zake kumaunika dziko.Dziko lapansi limaona zimenezi ndipo limanjenjemera.+
3 Moto umachoka kwa iye+Nʼkupsereza adani ake omuzungulira.+ 4 Kungʼanima kwa mphezi zake kumaunika dziko.Dziko lapansi limaona zimenezi ndipo limanjenjemera.+