Mateyu 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimene ndimakuuzani mumdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunongʼonezana, muzilalikire muli padenga.+
27 Zimene ndimakuuzani mumdima, muzinene poyera, ndipo zimene mumamva anthu akunongʼonezana, muzilalikire muli padenga.+