Salimo 33:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani! Diso la Yehova limayangʼana anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera chikondi chake chokhulupirika,19 Kuti awapulumutse ku imfa,Komanso kuwathandiza kuti akhale ndi moyo pa nthawi ya njala.+ Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ Mateyu 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho nthawi zonse muziika Ufumu ndi mfundo zolungama za Mulungu pamalo oyamba pa moyo wanu, ndipo iye adzakupatsani zinthu zina zonsezi.+
18 Taonani! Diso la Yehova limayangʼana anthu amene amamuopa,+Amene amayembekezera chikondi chake chokhulupirika,19 Kuti awapulumutse ku imfa,Komanso kuwathandiza kuti akhale ndi moyo pa nthawi ya njala.+
25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+
33 Choncho nthawi zonse muziika Ufumu ndi mfundo zolungama za Mulungu pamalo oyamba pa moyo wanu, ndipo iye adzakupatsani zinthu zina zonsezi.+