Salimo 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kwa munthu woyera, mumasonyeza kuti ndinu woyera,+Koma kwa munthu wopotoka maganizo mumasonyeza kuti ndinu wochenjera.+ Miyambo 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chifukwa Yehova amanyansidwa ndi munthu wachiphamaso,+Koma anthu owongoka mtima amakhala nawo pa ubwenzi wolimba.+
26 Kwa munthu woyera, mumasonyeza kuti ndinu woyera,+Koma kwa munthu wopotoka maganizo mumasonyeza kuti ndinu wochenjera.+
32 Chifukwa Yehova amanyansidwa ndi munthu wachiphamaso,+Koma anthu owongoka mtima amakhala nawo pa ubwenzi wolimba.+