-
1 Samueli 16:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Pamene iwo ankalowa, Samueli anaona Eliyabu+ ndipo anati: “Sindikukayikira, Yehova wasankha ameneyu.”* 7 Koma Yehova anauza Samueli kuti: “Usaganizire mmene akuonekera komanso kutalika kwake+ chifukwa ine ndamukana ameneyu. Chifukwatu mmene munthu amaonera si mmene Mulungu amaonera. Munthu amaona zooneka ndi maso, koma Yehova amaona mumtima.”+
-