Salimo 37:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ 26 Nthawi zonse amakongoza ena zinthu zake mokoma mtima,+Ndipo ana ake adzalandira madalitso. Salimo 112:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye wagawira ena mowolowa manja, wapereka kwa anthu osauka.+ צ [Tsade] Chilungamo chake chidzakhalapo mpaka kalekale.+ ק [Qoph] Mphamvu zake zidzawonjezeka* chifukwa cha ulemerero. Luka 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aliyense amene wakupempha kanthu mupatse,+ ndipo amene wakulanda zinthu usamuumirize kuti abweze.
25 Ndinali mwana ndipo tsopano ndakula,Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ 26 Nthawi zonse amakongoza ena zinthu zake mokoma mtima,+Ndipo ana ake adzalandira madalitso.
9 Iye wagawira ena mowolowa manja, wapereka kwa anthu osauka.+ צ [Tsade] Chilungamo chake chidzakhalapo mpaka kalekale.+ ק [Qoph] Mphamvu zake zidzawonjezeka* chifukwa cha ulemerero.