Salimo 119:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Zili bwino kuti ndakumana ndi mavuto,+Kuti ndiphunzire malamulo anu. Luka 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Osangalala ndinu amene mukumva njala, chifukwa mudzakhuta.+ Osangalala ndinu amene mukulira, chifukwa mudzaseka.+
21 Osangalala ndinu amene mukumva njala, chifukwa mudzakhuta.+ Osangalala ndinu amene mukulira, chifukwa mudzaseka.+