Salimo 141:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera. Miyambo 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Munthu amene amamvetsera chidzudzulo chopatsa moyo,Amakhala pakati pa anthu anzeru.+
5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza chikondi chokhulupirika.+Akandidzudzula zingakhale ngati wandidzoza mafuta pamutu,+Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+ Ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.