Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma sanasangalale ndi Kaini komanso nsembe yake ngakhale pangʼono. Choncho Kaini anapsa mtima kwambiri ndipo nkhope yake inagwa chifukwa cha chisoni.

  • Esitere 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pa tsikuli Hamani anatuluka ali wosangalala kwambiri. Koma atangoona Moredikayi pageti la mfumu nʼkuonanso kuti sanaimirire ndi kumunjenjemerera, Hamani anamukwiyira kwambiri Moredikayi.+

  • Miyambo 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Munthu amene amakwiya msanga amachita zinthu zopusa,+

      Koma munthu amene amaganiza bwino amadedwa.

  • Miyambo 14:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Munthu amene sakwiya msanga ndi wozindikira zinthu kwambiri,+

      Koma wosaugwira mtima amasonyeza uchitsiru wake.+

  • Miyambo 29:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu wopusa amatulutsa mkwiyo wake wonse,+

      Koma wanzeru amakhala wodekha ndipo amalamulira mkwiyo wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena