Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 1:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Mʼchaka choyamba cha Koresi+ mfumu ya Perisiya, pokwaniritsa mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa Yeremiya,+ Yehova analimbikitsa Koresi mfumu ya Perisiya kuti alengeze mu ufumu wake wonse, zomwenso iye analemba mʼmakalata,+ kuti:

      2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti, ‘Yehova Mulungu wakumwamba wandipatsa maufumu onse apadziko lapansi.+ Iye wandituma kuti ndimumangire nyumba ku Yerusalemu+ mʼdziko la Yuda.

  • Yesaya 44:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndine amene ndikunena za Koresi+ kuti, ‘Iye ndi mʼbusa wanga,

      Ndipo adzakwaniritsa bwinobwino zonse zimene ndikufuna,’+

      Amene ndanena zokhudza Yerusalemu kuti, ‘Adzamangidwanso,’

      Ndiponso zokhudza kachisi kuti, ‘Maziko ako adzamangidwa.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena