Genesis 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pachiyambi, Mulungu analenga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Yesaya 40:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi iwe sukudziwa? Kodi sunamve? Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi ndi Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angamvetse* nzeru zake.+
28 Kodi iwe sukudziwa? Kodi sunamve? Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi ndi Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angamvetse* nzeru zake.+