Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mulungu sali ngati munthu amene amanena mabodza,+

      Sali ngati mwana wa munthu amene amasintha maganizo.*+

      Akanena kanthu, kodi angalephere kuchita?

      Akalankhula, kodi angalephere kukwaniritsa?+

  • Yobu 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Akatsimikiza kuti achite zinthu, ndi ndani angamuletse?+

      Akafuna kuchita chinthu, amachitadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena