Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 21:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Palibe lonjezo* limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+

  • Yesaya 55:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mofanana ndi mvula komanso sinowo* zimene zimagwa kuchokera kumwamba

      Ndipo sizibwerera kumeneko mpaka zitanyowetsa kwambiri nthaka nʼkuchititsa kuti mbewu zimere ndi kubereka zipatso,

      Nʼkupereka mbewu kuti anthu adzale komanso chakudya kuti adye,

      11 Ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+

      Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+

      Koma adzachitadi chilichonse chimene ine ndikufuna,+

      Ndipo zimene ndinawatumizira kuti achite zidzachitikadi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena