Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu sali ngati munthu amene amanena mabodza,+Sali ngati mwana wa munthu amene amasintha maganizo.*+ Akanena kanthu, kodi angalephere kuchita? Akalankhula, kodi angalephere kukwaniritsa?+ Yesaya 46:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndikuitana mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa,*+Ndikuitana munthu kuchokera kudziko lakutali kuti adzachite zolinga zanga.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita. Ndakonza kuti zimenezi zichitike komanso ndidzazichita.+
19 Mulungu sali ngati munthu amene amanena mabodza,+Sali ngati mwana wa munthu amene amasintha maganizo.*+ Akanena kanthu, kodi angalephere kuchita? Akalankhula, kodi angalephere kukwaniritsa?+
11 Ine ndikuitana mbalame yodya nyama kuchokera kotulukira dzuwa,*+Ndikuitana munthu kuchokera kudziko lakutali kuti adzachite zolinga zanga.+ Ineyo ndalankhula ndipo ndidzazichita. Ndakonza kuti zimenezi zichitike komanso ndidzazichita.+