Yesaya 41:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Anthu ovutika ndi osauka akufunafuna madzi, koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma chifukwa cha ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+
17 “Anthu ovutika ndi osauka akufunafuna madzi, koma sakuwapeza. Lilime lawo lauma chifukwa cha ludzu.+ Ineyo Yehova ndidzawayankha.+ Ineyo Mulungu wa Isiraeli, sindidzawasiya.+