Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ‘Yehova ndi wosakwiya msanga, ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.*+ Amakhululukira zolakwa ndi machimo, koma sadzalekerera wolakwa osamupatsa chilango. Amalanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.’+

  • Salimo 103:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mofanana ndi mmene kotulukira dzuwa kwatalikirana ndi kolowera dzuwa,

      Mulungu waikanso zolakwa zathu kutali ndi ife.+

      13 Mofanana ndi bambo amene amasonyeza chifundo kwa ana ake,

      Yehova wasonyezanso chifundo kwa anthu amene amamuopa.+

  • Yesaya 43:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ineyo ndi amene ndikufafaniza zolakwa zako*+ chifukwa cha dzina langa,+

      Ndipo machimo ako sindidzawakumbukira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena