Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 50:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu wathu adzabwera ndipo sangakhale chete.+

      Pamaso pake pali moto wowononga,+

      Ndipo pamalo onse omuzungulira pali chimphepo chamkuntho.+

  • Salimo 50:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Utachita zinthu zimenezi, ine sindinalankhule kanthu,

      Choncho unkaganiza kuti ndikuona zinthu ngati mmene iweyo ukuzionera.

      Koma tsopano ndikudzudzula

      Ndipo ndikuuza mlandu umene ndakupeza nawo.+

  • Yeremiya 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choyamba ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse ndi machimo awo onse,+

      Chifukwa aipitsa dziko langa ndi zifaniziro zopanda moyo za mafano* awo onyansa

      Ndipo adzaza cholowa changa ndi zinthu zawo zonyansa.’”+

  • Ezekieli 11:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘“Koma amene atsimikiza mumtima mwawo kuti apitirize kutsatira mafano awo onyansa komanso kuchita zinthu zonyansa, ndidzawabwezera mogwirizana ndi zochita zawo,” akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena