Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Phiri la Sinai linafuka utsi paliponse, chifukwa chakuti Yehova anabwera paphiripo mʼmoto.+ Utsi wakewo unkakwera kumwamba ngati utsi wa uvuni ndipo phiri lonse linkanjenjemera kwambiri.+

  • Danieli 7:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndinapitiriza kuyangʼana mpaka pamene mipando yachifumu inaikidwa ndipo Wamasiku Ambiri+ anakhala pampando wake wachifumu.+ Zovala zake zinali zoyera kwambiri+ ndipo tsitsi lake linali looneka ngati ubweya wa nkhosa woyera. Mpando wake wachifumu unkaoneka ngati malawi a moto ndipo mawilo a mpandowo ankaoneka ngati moto umene ukuyaka.+ 10 Mtsinje wa moto unkayenda kuchokera kwa iye.+ Panali atumiki okwana 1 miliyoni* amene ankatumikira nthawi zonse ndi atumiki enanso 100 miliyoni* amene ankatumikira pamaso pake nthawi zonse.+ Bwalo la milandu+ linayamba kuzenga mlandu ndipo mabuku anatsegulidwa.

  • Aheberi 12:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Chifukwa Mulungu wathu ali ngati moto wowononga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena