Salimo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitunduyo udzaiphwanya ndi ndodo yachifumu yachitsulo,+Ndipo udzaiswa ngati chiwiya chadothi.”+ Salimo 110:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova adzatambasula ndodo yako yachifumu kuti ulamulirenso madera ena osati mu Ziyoni mokha. Iye adzanena kuti: “Pita pakati pa adani ako ndipo ukawagonjetse.”+ Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+ Chivumbulutso 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+
2 Yehova adzatambasula ndodo yako yachifumu kuti ulamulirenso madera ena osati mu Ziyoni mokha. Iye adzanena kuti: “Pita pakati pa adani ako ndipo ukawagonjetse.”+
11 Ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Amene anakwera pahatchiyo dzina lake linali lakuti Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iye amaweruza molungama ndipo akumenya nkhondo mwachilungamo.+
15 Mʼkamwa mwake munkatuluka lupanga lalitali+ lakuthwa, loti aphere mitundu ya anthu ndipo adzawakusa ndi ndodo yachitsulo.+ Komanso iye ankapondaponda muchopondera mphesa cha mkwiyo waukulu wa Mulungu Wamphamvuyonse.+