Yesaya 43:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+ Yeremiya 50:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova watsegula nyumba yake yosungiramo zida,Ndipo akutulutsamo zida zimene amagwiritsa ntchito posonyeza mkwiyo wake.+ Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, ali ndi ntchito yoti achiteMʼdziko la Akasidi. Yeremiya 51:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Wowononga adzafikira Babulo.+Asilikali ake adzagwidwa,+Mauta awo adzathyoledwa,Chifukwa Yehova ndi Mulungu amene amapereka chilango choyenera.+ Iye adzabwezera ndithu.+
14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+
25 Yehova watsegula nyumba yake yosungiramo zida,Ndipo akutulutsamo zida zimene amagwiritsa ntchito posonyeza mkwiyo wake.+ Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, ali ndi ntchito yoti achiteMʼdziko la Akasidi.
56 Wowononga adzafikira Babulo.+Asilikali ake adzagwidwa,+Mauta awo adzathyoledwa,Chifukwa Yehova ndi Mulungu amene amapereka chilango choyenera.+ Iye adzabwezera ndithu.+