Salimo 51:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeretseni ndi hisope* ku machimo anga kuti ndikhale woyera.+Ndisambitseni kuti ndiyere kwambiri kuposa matalala.+ Yesaya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+ Mika 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzagonjetsa* zolakwa zathu. Machimo athu onse mudzawaponya mʼnyanja pamalo ozama.+
7 Ndiyeretseni ndi hisope* ku machimo anga kuti ndikhale woyera.+Ndisambitseni kuti ndiyere kwambiri kuposa matalala.+
22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+
19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzagonjetsa* zolakwa zathu. Machimo athu onse mudzawaponya mʼnyanja pamalo ozama.+