Salimo 25:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wabwino komanso wolungama.+ Nʼchifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende mʼnjira yoyenera.+ י [Yod] 9 Adzatsogolera ofatsa kuti azichita zinthu zoyenera,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuti aziyenda mʼnjira yake.+
8 Yehova ndi wabwino komanso wolungama.+ Nʼchifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende mʼnjira yoyenera.+ י [Yod] 9 Adzatsogolera ofatsa kuti azichita zinthu zoyenera,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuti aziyenda mʼnjira yake.+