Salimo 119:165 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 165 Anthu amene amakonda chilamulo chanu amakhala ndi mtendere wochuluka,+Palibe chimene chingawakhumudwitse.* Yesaya 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+
165 Anthu amene amakonda chilamulo chanu amakhala ndi mtendere wochuluka,+Palibe chimene chingawakhumudwitse.*
12 Chifukwa mudzapita mukusangalala,+Ndipo adzakubweretsani kwanu mwamtendere.+ Mukadzafika, mapiri ndi zitunda zidzafuula mosangalala,+Ndipo mitengo yonse yakutchire idzawomba mʼmanja.+